CHIDZIWITSO

Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa anthu onse ogulitsa ndi kugula malonda osiyanasiya mu Msika waukulu otchedwa Mpanipani kuti, malo osungilapo magalimoto a pa Msikawu akhala otsekedwa kuyambila pa 1st January, 2021. Khonsoloyi idzakhala ikukonza malowa panthawiyi. Pa chifukwa ichi, Khonsoloyi ikudziwitsa anthu onse kuti azikasunga magalimoto awo kuseri kwa Msika wa Mpanipani moyang’anizana ndi … Continue reading CHIDZIWITSO