Kugawana ndi kugulitsana malo a Boma mu Mzinda wa Lilongwe
Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa anthu omwe akugawana ndikugulitsana malo mmadera osiyanasiyana mumzindawu kuti kutero ndikuphwanya malamulo a za malo (Land Act 2016) ndiponso a zomangamanga (Physical Planning Act 2016). Khonsoloyi ikuchenjeza iwo omwe akugulitsana ndi kugawana malo ndiponso kumanga mmalowa popanda chilolezo kuti Khonsolo ya Lilongwe idzachotsa katundu womangira (njerwa, mchenga, miyala ndi … Continue reading Kugawana ndi kugulitsana malo a Boma mu Mzinda wa Lilongwe
Copy and paste this URL into your WordPress site to embed
Copy and paste this code into your site to embed