Edit

About Us

The Lilongwe City Council was established under the Local Government Act No. 42 of 1998 as a body corporate. The Council comprises the Political and Administrative arms which both derive their authority from the Local Government Act of 1998. The Political  arm is led by the Mayor who is an elected councillor. The mayor is in charge of 27 Wards each overseen by an elected Councillor.  In addition, there are four (4) elected Members of Parliament who represent the Lilongwe urban sector. There are also five (5)  ex-official members representing interest groups. The Administrative arm of Lilongwe City Council is led by the Chief Executive Officer who oversees nine (9) technical departments and devolved sectors, including Commerce & Trade, Engineering, Education, Youth & Sports Sector, Parks & Recreation, Health and Social Welfare Services, Planning & Development and Finance.

Contact Info

Chidziwitso :  Tsiku Losesa, Kuchotsa Zinyalala ndi Kukonza malo

Chidziwitso : Tsiku Losesa, Kuchotsa Zinyalala ndi Kukonza malo

Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ikukumbutsa anthu onse mu mzindawu kuti tsiku losesa, kuchotsa zinyalala ndi kukonza malo mwezi uno likhalapo lero pa 11 February 2022 kuyambira nthawi ya 2 koloko masana mpaka 5 koloko madzulo.

Khonsoloyi ikupempha atsogoleli onse a: m’ma ofesi a boma, mabungwe oziyimira pa okha, makampani, a Mpingo, Makhansala, Mafumu ndi ena onse kuti azatsogolere ntchitoyi mumadera awo.

Khonsoloyi ikukumbutsanso anthu onse kuti azabweretse zipangizo zogwirira ntchitoyi monga masache, makasu, ndi zida zina zoyenelera; kuphatikizapo  zodzitchinjilizira kunkhope zoti adzagwilitse ntchito, ndikudzitetezera panthawiyi.

Dziwani kuti makampani kapena mabungwe ali ndi ufulu wosankha komwe afuna akagwire ntchitoyi; ndipo adziwitse mwansanga a Khonsoloyi.

Khonsoloyi ikukumbutsa anthu onse kuti azatsatire njira zonse zopewera matenda a Korona (Covid-19) pogwira ntchitoyi.

Kuti mudziwe zambiri imbirani foni a Thokozani Mkaka pa nambala iyi: 0999572208/0888572208 kapena a Benson Chidaomba pa nambala iyi: 0999375166.

Kumbukirani kuti kusunga ukhondo wa mzinda wa Lilongwe ndi udindo wa aliyense.

Lilongwe City Council

Subscribe Newsletter

Sign up for our latest news & articles. We won’t give you spam mails.

© 2020 Lilongwe City Council. All Rights Reserved