Edit

About Us

The Lilongwe City Council was established under the Local Government Act No. 42 of 1998 as a body corporate. The Council comprises the Political and Administrative arms which both derive their authority from the Local Government Act of 1998. The Political  arm is led by the Mayor who is an elected councillor. The mayor is in charge of 27 Wards each overseen by an elected Councillor.  In addition, there are four (4) elected Members of Parliament who represent the Lilongwe urban sector. There are also five (5)  ex-official members representing interest groups. The Administrative arm of Lilongwe City Council is led by the Chief Executive Officer who oversees nine (9) technical departments and devolved sectors, including Commerce & Trade, Engineering, Education, Youth & Sports Sector, Parks & Recreation, Health and Social Welfare Services, Planning & Development and Finance.

Contact Info

Kusamuka kwa msika wa nsomba zouma kuchoka ku msika waukulu wa mpanipani kupita ku dela la 25B

Kusamuka kwa msika wa nsomba zouma kuchoka ku msika waukulu wa mpanipani kupita ku dela la 25B

khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa onse okhala mu mzindawu  zakusamuka kwa msika waukulu  wa msomba zouma  ku mpanipani  kupita ku msika wa 25B. izi zachitika pa zifukwa izi:

  1. Kufuna kuchepetsa kuthithikana kwa anthu mu msika ngati njira imodzi yopewera kufalikira kwa kachilombo koyambitsa matenda a Covid-19.
  2. Kufuna kuwonjezera malo osungirapo galimoto zimene zithandizire kuchepetsa kuthithikana kwa njira zodutsa magalimotowa.
  3. Kufuna kuonjezera nthawi yochitira malondawa kwa anthu ogulitsa nsomba zouma kuti azitha kugulitsa tsiku lonse komanso kuti akhale kufupi ndi malo opikulira nsomba. 

Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ikupempha ogulitsa nsomba ndi onse ogula nsomba kuti atsatire ndondomeko imene yakhazikitsidwayi.

Lilongwe City Council

Subscribe Newsletter

Sign up for our latest news & articles. We won’t give you spam mails.

© 2020 Lilongwe City Council. All Rights Reserved