Edit

About Us

The Lilongwe City Council was established under the Local Government Act No. 42 of 1998 as a body corporate. The Council comprises the Political and Administrative arms which both derive their authority from the Local Government Act of 1998. The Political  arm is led by the Mayor who is an elected councillor. The mayor is in charge of 27 Wards each overseen by an elected Councillor.  In addition, there are four (4) elected Members of Parliament who represent the Lilongwe urban sector. There are also five (5)  ex-official members representing interest groups. The Administrative arm of Lilongwe City Council is led by the Chief Executive Officer who oversees nine (9) technical departments and devolved sectors, including Commerce & Trade, Engineering, Education, Youth & Sports Sector, Parks & Recreation, Health and Social Welfare Services, Planning & Development and Finance.

Contact Info

NEWS

Kwa onse ochita malonda m’malo osavomerezeka ndi khonsolo

May 22, 2021

Kwa onse ochita malonda m’malo osavomerezeka ndi khonsolo

Mukukumbutsidwa kuti kuchita malonda m’malo osavomerezeka ndikhonsolo ngati mphepete mwamisewu ndimalo ena otero ndikuphwanya malamulo a Khonsolo. Motero, Khonsolo ya Lilongwe ikudziwitsa onse  ochita malonda m’malo osavomelezedwawa kuti achoke.   Khonsoloyi

01
Kuletsa kabaza wa Njinga za moto ndi
zakapalasa mmadera ndi misewu ikuluikulu
mu mzinda wa Lilongwe

May 21, 2021

Kuletsa kabaza wa Njinga za moto ndi
zakapalasa mmadera ndi misewu ikuluikulu
mu mzinda wa Lilongwe

Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa  a kabaza wakapalasa ndi wa njinga zamoto  onse kuti ndikoletsedwa kuchita malonda awo mumzindawu  mmalo aku Old Town, City Centre ndiponso misewu yonse ikuikulu

02
KUBA NDIKUWONONGA KATUNDU WA BOMA

May 15, 2021

KUBA NDIKUWONONGA KATUNDU WA BOMA

Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ndi yokhudzidwa ndi mchitidwe womwe mzika zina za mzindawu zikuchita pokuba ndikuononga nyali zamu nseu, mawaya a nyali zothandizila magalimoto ndi anthu pa mseu ndi

03
Request for Expressions of Interest for
the Flagship Projects for Lilongwe City

May 10, 2021

Request for Expressions of Interest for
the Flagship Projects for Lilongwe City

Background Lilongwe City Council (The Council) was established by an Act of Parliament (The Local Government 2010 Amended). The Act mandates the Council to provide services to the City Residents.

05
Kusamuka kwa msika wa nsomba zouma kuchoka ku msika waukulu wa mpanipani kupita ku dela la 25B

April 15, 2021

Kusamuka kwa msika wa nsomba zouma kuchoka ku msika waukulu wa mpanipani kupita ku dela la 25B

khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa onse okhala mu mzindawu  zakusamuka kwa msika waukulu  wa msomba zouma  ku mpanipani  kupita ku msika wa 25B. izi zachitika pa zifukwa izi: Kufuna

06

Lilongwe City Council

Subscribe Newsletter

Sign up for our latest news & articles. We won’t give you spam mails.

© 2020 Lilongwe City Council. All Rights Reserved