Edit

About Us

The Lilongwe City Council was established under the Local Government Act No. 42 of 1998 as a body corporate. The Council comprises the Political and Administrative arms which both derive their authority from the Local Government Act of 1998. The Political  arm is led by the Mayor who is an elected councillor. The mayor is in charge of 27 Wards each overseen by an elected Councillor.  In addition, there are four (4) elected Members of Parliament who represent the Lilongwe urban sector. There are also five (5)  ex-official members representing interest groups. The Administrative arm of Lilongwe City Council is led by the Chief Executive Officer who oversees nine (9) technical departments and devolved sectors, including Commerce & Trade, Engineering, Education, Youth & Sports Sector, Parks & Recreation, Health and Social Welfare Services, Planning & Development and Finance.

Contact Info

Kwa onse ochita malonda m’malo osavomerezeka ndi khonsolo

Kwa onse ochita malonda m’malo osavomerezeka ndi khonsolo

Mukukumbutsidwa kuti kuchita malonda m’malo osavomerezeka ndikhonsolo ngati mphepete mwamisewu ndimalo ena otero ndikuphwanya malamulo a Khonsolo.

Motero, Khonsolo ya Lilongwe ikudziwitsa onse  ochita malonda m’malo osavomelezedwawa kuti achoke. 

 Khonsoloyi ikhala ikuchotsa onse omwe akupangira malonda m’malo osavomerezedwawa.  Aliyense yemwe adzapezeke akupitiriza kuchita malonda m’malowa adzalipiritsidwa chindapusa ndikulandidwa malonda akewo ngakhale kumangidwa kumene.

 Tiyeni tonse tikonde mzinda wathu kuti ukhale wosililika ndi wadongosolo pochitira malonda athu m’malo omwe a khonsolo avomeleza.  Komanso  tonse ogula malonda tiyeni tipewe kugula zinthu zogulitsidwa m’malo achisawawa. 

Mukafuna kudziwa zambiri tipezeni motere: tilembereni ku info@lcc.mw   kapena kuyimba ku nambala ya ulele ya 346.  

Eliam Banda

M’malo mwa Mkulu Woyang’anira Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe

Lilongwe City Council

Subscribe Newsletter

Sign up for our latest news & articles. We won’t give you spam mails.

© 2020 Lilongwe City Council. All Rights Reserved