Edit

About Us

The Lilongwe City Council was established under the Local Government Act No. 42 of 1998 as a body corporate. The Council comprises the Political and Administrative arms which both derive their authority from the Local Government Act of 1998. The Political  arm is led by the Mayor who is an elected councillor. The mayor is in charge of 27 Wards each overseen by an elected Councillor.  In addition, there are four (4) elected Members of Parliament who represent the Lilongwe urban sector. There are also five (5)  ex-official members representing interest groups. The Administrative arm of Lilongwe City Council is led by the Chief Executive Officer who oversees nine (9) technical departments and devolved sectors, including Commerce & Trade, Engineering, Education, Youth & Sports Sector, Parks & Recreation, Health and Social Welfare Services, Planning & Development and Finance.

Contact Info

CHIDZIWITSO

CHIDZIWITSO

Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa anthu onse ogulitsa ndi kugula malonda osiyanasiya mu Msika waukulu otchedwa Mpanipani kuti, malo osungilapo magalimoto a pa Msikawu akhala otsekedwa kuyambila pa 1st January, 2021. Khonsoloyi idzakhala ikukonza malowa panthawiyi.

Pa chifukwa ichi, Khonsoloyi ikudziwitsa anthu onse kuti azikasunga magalimoto awo kuseri kwa Msika wa Mpanipani moyang’anizana ndi Mogasa, komaso pa Tikambe mu mseu wa Malangalanga moyang’anizana ndi ma ofesi a khonsoloyi ku Chidzanja kapena mphepete mwa malo ochitira malonda a U-Save ndi K99 ku old town.

Malowa adzakhala otseka chomwechi kwa masabata anayi (4).

Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikupepesa kwa onse okhudzidwa ndi kutseka kwa malowa.

Lilongwe City Council

Subscribe Newsletter

Sign up for our latest news & articles. We won’t give you spam mails.

© 2020 Lilongwe City Council. All Rights Reserved