In a bid to improve communication between Lilongwe city council (LCC) and ratepayers in the city, Lilongwe city council is requesting you to send the following important details: Your name Name of your business or property Plot number Contact details…
Lilongwe Water Board (LWB) in conjunction with Lilongwe City Council (LCC) wishes to inform the general public that it has introduced “ZAMAKONO” as the new visual imagery in implementation of the Lilongwe Water and Sanitation Project (LWSP) funded by World…
Mukukumbutsidwa kuti kuchita malonda m’malo osavomerezeka ndikhonsolo ngati mphepete mwamisewu ndimalo ena otero ndikuphwanya malamulo a Khonsolo. Motero, Khonsolo ya Lilongwe ikudziwitsa onse ochita malonda m’malo osavomelezedwawa kuti achoke. Khonsoloyi ikhala ikuchotsa onse omwe akupangira malonda m’malo osavomerezedwawa. Aliyense yemwe…
Khonsolo ya Mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa a kabaza wakapalasa ndi wa njinga zamoto onse kuti ndikoletsedwa kuchita malonda awo mumzindawu mmalo aku Old Town, City Centre ndiponso misewu yonse ikuikulu mumzindawu. Aliyense yemwe adzapezeke akuyendetsa kabaza wakapalasa kapena wa njinga…
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ndi yokhudzidwa ndi mchitidwe womwe mzika zina za mzindawu zikuchita pokuba ndikuononga nyali zamu nseu, mawaya a nyali zothandizila magalimoto ndi anthu pa mseu ndi zikwangwani za m’miseu. Izi zikuchitika kwambiri madera awa: area18, 25…
Background Lilongwe City Council (The Council) was established by an Act of Parliament (The Local Government 2010 Amended). The Act mandates the Council to provide services to the City Residents. The Council is composed of the political and administrative structure.…
khonsolo ya mzinda wa Lilongwe ikudziwitsa onse okhala mu mzindawu zakusamuka kwa msika waukulu wa msomba zouma ku mpanipani kupita ku msika wa 25B. izi zachitika pa zifukwa izi: Kufuna kuchepetsa kuthithikana kwa anthu mu msika ngati njira imodzi yopewera…
For more details click on the download button below.
Intro. The world is in the midst of a COVID-19 pandemic. As World Health Organization (WHO) and partners work together on the response — tracking the pandemic, advising on critical interventions, distributing vital medical supplies to those in need— they…